Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • ll gawo 10 tsamba 22-23
  • Kodi Anthu Omvera Mulungu Adzalandira Madalitso Otani?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Anthu Omvera Mulungu Adzalandira Madalitso Otani?
  • Mverani Mulungu Kuti Mudzapeze Moyo Wosatha
  • Nkhani Yofanana
  • Chigawo 10
    Mverani Mulungu
  • “Taonani! Zinthu Zonse Zimene Ndikupanga N’zatsopano”
    Nsanja ya Olonda—2013
  • Mabwenzi a Mulungu Adzakhala M’paradaiso
    Mungathe Kukhala Bwenzi la Mulungu!
  • Kodi Chifuno cha Mulungu cha Dziko Lapansi N’chiyani?
    Kodi Mulungu Amafunanji kwa Ife?
Onani Zambiri
Mverani Mulungu Kuti Mudzapeze Moyo Wosatha
ll gawo 10 tsamba 22-23

CHIGAWO 10

Kodi Anthu Omvera Mulungu Adzalandira Madalitso Otani?

Ambiri mwa anthu amene anamwalira adzaukitsidwa padziko lapansi. Machitidwe 24:15

Anthu anthu ali m’Paradaiso ndipo akulandira anzawo amene aukitsidwa

Pali madalitso ambiri amene mudzalandire m’tsogolo muno ngati mukumvera Yehova. Mudzakhala ndi thanzi labwino ndipo palibe amene adzadwale, kulumala kapena kukalamba. Mudzatha kukhulupirira munthu aliyense chifukwa sikudzakhala anthu oipa.

Sikudzakhala zinthu zilizonse zopweteka, chisoni kapenanso kulira. Palibe amene adzakalambe ndi kufa.

Mudzasangalala kukhala pamodzi ndi anzanu komanso achibale anu ndipo moyo udzakhala wosangalatsa kwambiri m’Paradaiso.

Anthu adzakhala mopanda mantha ndipo adzakhaladi osangalala.

Ufumu wa Mulungu udzathetsa mavuto onse. Chivumbulutso 21:3, 4

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena