Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • lfb tsamba 58-59
  • Mawu Oyamba Gawo 5

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mawu Oyamba Gawo 5
  • Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • Nkhani Yofanana
  • Kupindula ndi “Tirigu wa Kumwamba”
    Nsanja ya Olonda—1999
  • Mawu Oyamba Gawo 11
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • Mawu Oyamba Gawo 4
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • Analonjeza Kuti Azimvera Yehova
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
Onani Zambiri
Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
lfb tsamba 58-59
Aisiraeli akutola mana

Mawu Oyamba Gawo 5

Patangotha miyezi iwiri kuchokera pamene anawoloka Nyanja Yofiira, Aisiraeli anafika paphiri la Sinai. Paphirili, Yehova anachita nawo pangano loti akhale anthu ake apadera. Iye ankawateteza komanso kuwapatsa zofunika pa moyo. Ankawapatsa malo abwino oti azikhala, chakudya chotchedwa mana komanso zovala zawo sizinkatha. Ngati ndinu kholo, thandizani mwana wanu kudziwa chifukwa chake Yehova anapatsa Aisiraeli Chilamulo, chihema komanso ansembe. Tsindikani ubwino wochita zimene talonjeza, kukhala odzichepetsa komanso okhulupirika kwa Yehova.

ZIMENE TIPHUNZIRE M’CHIGAWOCHI

  • Tiziyesetsa kuchita zimene talonjeza kwa Yehova

  • Kudzikuza, dyera komanso kusamvera zimabweretsa mavuto

  • Yehova ankachita zinthu ndi Aisiraeli moleza mtima ndipo ankawasamalira ngakhale kuti anali osakhulupirika

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena