Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • lfb tsamba 174-175
  • Mawu Oyamba Gawo 12

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mawu Oyamba Gawo 12
  • Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • Nkhani Yofanana
  • Yesu Atiphunzitsa Ife Kupemphera
    Kumamumvetsera Mphunzitsi Wamkuru’yo
  • Pankhani ya Mapemphero Amene Mulungu Amamva
    Nsanja ya Olonda—2009
  • “Ambuye, Tiphunzitseni Ife Kupemphera”
    Nsanja ya Olonda—2004
  • Choonadi Chonena za Ufumu wa Mulungu
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2020
Onani Zambiri
Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
lfb tsamba 174-175
Yesu akuphunzitsa akuluakulu ndi ana omwe

Mawu Oyamba Gawo 12

Yesu anaphunzitsa anthu zokhudza Ufumu wakumwamba. Iye anawaphunzitsanso kuti azipemphera kuti dzina la Mulungu liyeretsedwe, Ufumu wake ubwere komanso kuti zimene Mulungu amafuna zichitike padzikoli. Ngati ndinu kholo, fotokozerani mwana wanu chifukwa chake pempheroli ndi lofunika kwa ife. Yesu sanalole kuti Satana amulepheretse kukhala wokhulupirika kwa Mulungu. Iye anasankha atumwi ake ndipo iwo ndi amene anali oyamba kusankhidwa kuti adzalamulire nawo mu Ufumu. Thandizani mwana wanuyo kuti aone zoti Yesu anali wodzipereka kwambiri pa kulambira koona. Popeza Yesu ankafuna kuthandiza anthu anachiritsa odwala, anadyetsa anjala komanso anaukitsa akufa. Zinthu zodabwitsa zimene anachitazi zinasonyeza zimene Ufumu wa Mulungu udzachitire anthu.

ZIMENE TIPHUNZIRE M’CHIGAWOCHI

  • Yesu anauza otsatira ake kuti azilalikira za Ufumu komanso azithandiza anthu kuti akhale ophunzira ake

  • Popemphera, tizinena kaye zinthu zokhudza Yehova tisanapemphe zokhudza ifeyo

  • Tizikhululuka ndi mtima wonse ndiponso tizichitira anthu zimene tingafune kuti iwowo atichitire

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena