Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 93
  • Mudalitse Msonkhano Wathu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mudalitse Msonkhano Wathu
  • Imbirani Yehova Mosangalala
  • Nkhani Yofanana
  • Dalitsani Msonkhano Wathu!
    Imbirani Yehova
  • Dalitsani Kusonkhana Kwathu Pamodzi
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Kuyamikira Kudekha kwa Mulungu
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Kutamanda Mulungu Wathu Mfumu
    Imbirani Yehova Zitamando
Onani Zambiri
Imbirani Yehova Mosangalala
sjj nyimbo 93

NYIMBO 93

Mudalitse Msonkhano Wathu

Losindikizidwa

(Aheberi 10:​24, 25)

  1. 1. Pamsonkhanowu Yehova

    Chonde mutidalitse.

    Mutipatse mzimu wanu.

    Zikomo tasonkhana.

  2. 2. Mutithandize kumvetsa

    Mfundo za choonadi.

    Tizilalikira ena.

    Tikhale a chikondi.

  3. 3. Mudalitse msonkhanowu.

    Mutipatse mtendere.

    Mawu ndi zochita zathu

    Zikulemekezeni.

(Onaninso Sal. 22:22; 34:3; Yes. 50:4.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena