Loweruka
“[Kuonetsa] kulimba mtima kowonjezereka polankhula mawu a Mulungu mopanda mantha”—AFILIPI 1:14
M’MAWA
9:20 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
9:30 Nyimbo Na. 76 ndi Pemphero
9:40 NKHANI YOSIYIRANA: Muzichita Zinthu Molimba Mtima
Amene Mukuphunzira Baibulo (Machitidwe 8:35, 36; 13:48)
Achinyamata (Salimo 71:5; Miyambo 2:11)
Ofalitsa (1 Atesalonika 2:2)
Amene Muli pa Banja (Aefeso 4:26, 27)
Makolo (1 Samueli 17:55)
Apainiya (1 Mafumu 17:6-8, 12, 16)
Akulu (Machitidwe 20:28-30)
Achikulire (Danieli 6:10, 11; 12:13)
10:50 Nyimbo Na. 119 ndi Zilengezo
11:00 NKHANI YOSIYIRANA: Musamatsanzire Anthu Amantha, Koma Olimba Mtima
Osati Atsogoleri 10, Koma Yoswa ndi Kalebe (Numeri 14:7-9)
Osati Anthu a ku Merozi, Koma Yaeli (Oweruza 5:23)
Osati Aneneri Onyenga, Koma Mikaya (1 Mafumu 22:14)
Osati Uliya, Koma Yeremiya (Yeremiya 26:21-23)
Osati Wolamulira Wachinyamata, Koma Paulo (Maliko 10:21, 22)
11:45 NKHANI YA UBATIZO: “Ife Si Mtundu wa Anthu Obwerera M’mbuyo” (Aheberi 10:35, 36, 39; 11:30, 32-34, 36; 1 Petulo 5:10)
12:15 Nyimbo Na. 38 ndi Kupuma
MASANA
1:35 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
1:45 Nyimbo Na. 111
1:50 NKHANI YOSIYIRANA: Phunzirani Kulimba Mtima Kuchokera ku Zinthu za M’chilengedwe
Mikango (Mika 5:8)
Mahatchi (Yobu 39:19-25)
Msulu (Salimo 91:3, 13-15)
Choso (1 Petulo 3:15)
Njovu (Miyambo 17:17)
2:40 Nyimbo Na. 60 ndi Zilengezo
2:50 NKHANI YOSIYIRANA: Mmene Abale Athu Akusonyezera Kulimba Mtima
Ku Africa (Mateyu 10:36-39)
Ku Asia (Zekariya 2:8)
Ku Europe (Chivumbulutso 2:10)
Ku North America (Yesaya 6:8)
Ku Oceania (Salimo 94:14, 19)
Ku South America (Salimo 34:19)
4:15 Olimba Mtima Koma Osati Odzidalira (Miyambo 3:5, 6; Yesaya 25:9; Yeremiya 17:5-10; Yohane 5:19)
4:50 Nyimbo Na. 3 ndi Pemphero Lomaliza