Muzikonda Yehova Ndi Mtima Wanu Wonse
M’MAWA
9:40 Kumvetsera Nyimbo
9:50 Nyimbo Na. 109 ndi Pemphero
10:00 “Kukonda Mulungu Kumatanthauza Kusunga Malamulo Ake”
10:15 Amene Amakonda Yehova Amakondanso M’bale Wake
10:30 “Uzikonda Mnzako Mmene Umadzikondera Wekha”
10:55 Nyimbo Na. 82 ndi Zilengezo
11:05 “Chikondi Chimakwirira Machimo Ochuluka”
11:35 Kudzipereka Ndiponso Kubatizidwa
12:05 Nyimbo Na. 50
MASANA
1:20 Kumvetsera Nyimbo
1:30 Nyimbo Na. 62
1:35 Zochitika pa Moyo Wachikhristu
1:45 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda
2:15 Nkhani Yosiyirana: Muzitamanda Yehova Nthawi Yonse ya Moyo Wanu
Ana
Achinyamata
Akuluakulu
3:00 Nyimbo Na. 10 ndi Zilengezo
3:10 Muzikonda Yehova ndi Mtima Wanu Wonse
3:55 Nyimbo Na. 37 ndi Pemphero