‘Imvani Zimene Mzimu Ukunena ku Mipingo’
M’mawa
8:40 Kumvetsera Nyimbo
8:50 Nyimbo Na. 1 ndi Pemphero
9:00 Kodi Tingamve Bwanji “Zimene Mzimu Ukunena?”
9:15 “Sunafooke”
9:30 “Usachite Mantha”
9:55 Nyimbo Na. 73 ndi Zilengezo
10:05 “Sunakane Kuti Umandikhulupirira”
10:35 Nkhani ya Ubatizo: N’chifukwa Chiyani Mukubatizidwa?
11:05 Nyimbo Na. 79
Masana
12:20 Kumvetsera Nyimbo
12:30 Nyimbo Na. 126
12:35 Zochitika pa Moyo wa Chikhristu
12:45 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda
13:15 Nkhani Yosiyirana: Mmene Tingagwiritsire Ntchito Malangizo
• “Gwirani Mwamphamvu Zinthu Zabwino Zimene Muli Nazo”
• ‘Khala Maso, Ndipo Khala Olimba’
• “Ndatsegula Khomo Pamaso Pako”
14:00 Nyimbo Na. 76 ndi Zilengezo
14:10 ‘Khalani Odzipereka’
14:55 Nyimbo Na. 129 ndi Pemphero