Mupeze Mayankho A Mafunso Awa:
Kodi chikondi chimaposa bwanji kudziwa zinthu? (1 Akor. 8:1)
Kodi tingatani kuti tizilimbikitsa Akhristu anzathu ngati mmene atumiki a Mulungu akale ankachitira? (Aroma 13:8)
Kodi tingapereke bwanji moyo wathu kwa anthu mu utumiki? (1 Ates. 2:7, 8)
Kodi tingathandize bwanji kuti mpingo wachikhristu ukhale wolimba? (Aef. 4:1-3, 11-16; 1 Ates. 5:11)
Kodi tingatani kuti zonse zimene tikuchita, tizizichita mwachikondi? (1 Akor. 16:14)
© 2019 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania