Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • CA-brpgm25 tsamba 4
  • Mupeze Mayankho a Mafunso Awa

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mupeze Mayankho a Mafunso Awa
  • Pulogalamu ya Msonkhano Wadera Wokhala ndi Woimira Nthambi wa 2024-2025
  • Nkhani Yofanana
  • Mupeze Mayankho a Mafunso Awa
    Pulogalamu ya Msonkhano Wadera Wokhala ndi Woyang’anira Dera wa 2024-2025
  • Mupeze Mayankho a Mafunso Awa
    Pulogalamu ya Msonkhano Wadera Wokhala ndi Woimira Nthambi wa 2023-2024
  • Onesiforo—Wotonthoza Wolimba Mtima
    Nsanja ya Olonda—1997
  • Mupeze Mayankho a Mafunso Awa
    Pulogalamu ya Msonkhano Wadera wa 2019-2020—Wokhala ndi Woyang’anira Dera
Onani Zambiri
Pulogalamu ya Msonkhano Wadera Wokhala ndi Woimira Nthambi wa 2024-2025
CA-brpgm25 tsamba 4

Mupeze Mayankho a Mafunso Awa:

  1. 1. N’chifukwa chiyani ‘sitichita manyazi ndi uthenga wabwino’? (Aroma 1:16; 11:13)

  2. 2. Kodi timasonyeza bwanji kuti tili kumbali ya choonadi? (Mat. 10:32; Aroma 10:9)

  3. 3. Kodi n’chiyani chimatithandiza kuti tizilalikira bwino tikakhala mu utumiki? (2 Tim. 2:15)

  4. 4. Kodi tingatsanzire bwanji Onesiforo? (2 Tim. 1:​7, 8)

  5. 5. Kodi timasonyeza bwanji kuti sitichita manyazi kukhala kumbali ya Mulungu wathu? (Aheb. 10:39; 1 Pet. 3:15; Yoh. 18:36; 1 Ates. 5:​12, 13)

  6. 6. Kodi ‘timadzitama bwanji mwa Yehova’? (Sal. 34:​1, 2; 1 Akor. 1:31)

© 2024 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

CA-brpgm25-CN

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena