Loweruka
“Tsiku ndi tsiku muzilengeza uthenga wabwino wa chipulumutso chake”—Salimo 96:2
M’mawa
8:20 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
8:30 Nyimbo Na. 53 Komanso Pemphero
8:40 ‘Ndikuyenera . . . Kulengeza Uthenga Wabwino wa Ufumu’ (Luka 4:43)
8:50 VIDIYO:
Uthenga Wabwino wa Yesu: Gawo 1
Kuwala Kwenikweni kwa Dziko—Mbali Yachiwiri (Mateyu 2:1-23; Luka 2:1-38, 41-52; Yohane 1:9)
9:25 Nyimbo Na. 69 Komanso Zilengezo
9:35 NKHANI YOSIYIRANA: Kukwaniritsidwa kwa Maulosi Onena za Mesiya
• Kunabwera Mthenga Iye Asanabwere (Malaki 3:1; 4:5; Mateyu 11:10-14)
• Anabadwa kwa Namwali (Yesaya 7:14; Mateyu 1:18, 22, 23)
• Anabadwira ku Betelehemu (Mika 5:2; Luka 2:4-7)
• Anatetezedwa Ali Mwana (Hoseya 11:1; Mateyu 2:13-15)
• Anatchedwa Mnazareti (Yesaya 11:1, 2; Mateyu 2:23)
• Anaonekera pa Nthawi Yoikidwiratu (Danieli 9:25; Luka 3:1, 2, 21, 22)
10:40 NKHANI YA UBATIZO: Pitirizani ‘Kugonjera Uthenga Wabwino’ (2 Akorinto 9:13; 1 Timoteyo 4:12-16; Aheberi 13:17)
11:10 Nyimbo Na. 24 Komanso Kupuma
Masana
12:35 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
12:45 Nyimbo Na. 83
12:50 NKHANI YOSIYIRANA: Muzigwiritsa Ntchito Uthenga Wabwino Kuti Mugonjetse Uthenga Oipa
• Miseche (Yesaya 52:7)
• Kuvutika ndi Chikumbumtima (1 Yohane 1:7, 9)
• Zochitika za Masiku Ano (Mateyu 24:14)
• Zinthu Zofooketsa (Mateyu 11:28-30)
1:35 NKHANI YOSIYIRANA: ‘Muzikhala Ofunitsitsa Kulalikira Uthenga Wabwino’
• Sinali Ntchito ya Atumwi Okha (Aroma 1:15; 1 Atesalonika 1:8)
• Ndi Mbali ya Kulambira (Aroma 1:9)
• Muzikonzekera Komanso Kugwiritsa Ntchito Zinthu Zoyenera (Aefeso 6:15)
2:15 VIDIYO: Mmene ‘Uthenga Wabwino Ukubalira Zipatso Komanso Kufalikira Padziko Lonse’ (Akolose 1:6)
2:40 Nyimbo Na. 35 Komanso Zilengezo
2:50 NKHANI YOSIYIRANA: Pitirizani Kulalikira Uthenga Wabwino
• Kulikonse Komwe Muli (2 Timoteyo 4:5)
• Kulikonse Komwe Mulungu Akufuna (Machitidwe 16:6-10)
3:15 Kodi Mudzachita Chiyani “Chifukwa cha Uthenga Wabwino”? (1 Akorinto 9:23; Yesaya 6:8)
3:50 Nyimbo Na. 21 Komanso Pemphero Lomaliza