Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • CO-pgm24 tsamba 2-6
  • Lachisanu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Lachisanu
  • Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2024
  • Nkhani Yofanana
  • Lachisanu
    Pulogalamu ya Msonkhano wa 2025
  • Loweruka
    Pulogalamu ya Msonkhano wa 2025
  • Lamlungu
    Pulogalamu ya Msonkhano wa 2025
  • Loweruka
    Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2024
Onani Zambiri
Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2024
CO-pgm24 tsamba 2-6
Zithunzi: Zimene zili mupulogalamu ya Lachisanu. 1. M’nyumba yopatulika yapakachisi, mngelo akulankhula ndi Zekariya amene ali ndi mantha kwambiri. 2. Namwali Wachiyuda Mariya akuoneka wodabwa. 3. Yosefe ndi Mariya akuyenda ndi bulu. Mariya wanyamula Yesu.

Lachisanu

“Uthenga wabwino wa chimwemwe chachikulu chimene anthu onse adzakhale nacho”​—Luka 2:10

M’mawa

  • 8:20 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo

  • 8:30 Nyimbo Na. 150 Komanso Pemphero

  • 8:40 NKHANI YA TCHEYAMANI: N’chifukwa Chiyani Tikufunikira Uthenga Wabwino? (1 Akorinto 9:16; 1 Timoteyo 1:12)

  • 9:10 VIDIYO:

    Uthenga Wabwino wa Yesu: Gawo 1

    Kuwala Kwenikweni kwa Dziko​—Mbali Yoyamba (Mateyu 1:18-25; Luka 1:1-80; Yohane 1:1-5)

  • 9:45 Nyimbo Na. 96 Komanso Zilengezo

  • 9:55 NKHANI YOSIYIRANA: ‘Anatsogoleredwa ndi Mzimu Woyera’

    • • Mateyu (2 Petulo 1:21)

    • • Maliko (Maliko 10:21)

    • • Luka (Luka 1:1-4)

    • • Yohane (Yohane 20:31)

  • 11:10 Nyimbo Na. 110 Komanso Kupuma

Masana

  • 12:35 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo

  • 12:45 Nyimbo Na. 117

  • 12:50 NKHANI YOSIYIRANA: Muzikhulupirira Choonadi Chokhudza Yesu

    • • Mawu (Yohane 1:1; Afilipi 2:8-11)

    • • Dzina Lake (Machitidwe 4:12)

    • • Kubadwa Kwake (Mateyu 2:1, 2, 7-12, 16)

  • 1:30 Nyimbo Na. 99 Komanso Zilengezo

  • 1:40 NKHANI YOSIYIRANA: Zomwe Tikuphunzira pa Moyo wa M’nthawi ya Yesu

    • • Malo (Deuteronomo 8:7)

    • • Nyama (Luka 2:8, 24)

    • • Chakudya (Luka 11:3; 1 Akorinto 10:31)

    • • Moyo Wapakhomo (Afilipi 1:10)

    • • Moyo Wapamudzi (Deuteronomo 22:4)

    • • Maphunziro (Deuteronomo 6:6, 7)

    • • Kulambira (Deuteronomo 16:15, 16)

  • 3:15 N’chifukwa Chiyani Uthenga Wabwino Umatchulidwa Kuti ndi ‘Uthenga Wosatha’? (Chivumbulutso 14:6, 7)

  • 3:50 Nyimbo Na. 66 Komanso Pemphero Lomaliza

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena