‘Muzilambira Motsogoleredwa Ndi Mzimu Komanso Choonadi’
M’mawa
8:40 Kumvetsera Nyimbo
8:50 Nyimbo Na. 85 ndi Pemphero
9:00 “Atate Akufuna Anthu Ngati Amenewo”
9:15 Nkhani Yosiyirana: ‘Muzilambira Motsogoleredwa Ndi Mzimu’
• Mukamayesetsa Kuti Mumvetse Malangizo a Yehova
• Mukakhumudwa
• Mukamafuna Kuti Muzichita Zambiri Potumikira Yehova
10:05 Nyimbo Na. 88 ndi Zilengezo
10:15 Kodi ‘Timachititsa Bwanji Choonadi Kuti Chidziwike’?
10:35 Nkhani ya Ubatizo: N’chifukwa Chiyani Mukubatizidwa?
11:05 Nyimbo Na. 51
Masana
12:20 Kumvetsera Nyimbo
12:30 Nyimbo Na. 72 ndi Pemphero
12:35 Nkhani ya Onse: Kodi Tingadziwe Bwanji Zoyenera ndi Zosayenera?
13:05 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda
13:35 Nyimbo Na. 56 ndi Zilengezo
13:45 Nkhani Yosiyirana: ‘Muzilambira Motsogoleredwa Ndi Choonadi’
• M’banja
• M’dziko Logawanikali
• Mukakhala pa Mavuto Azachuma
14:30 “Gula Choonadi Ndipo Usachigulitse”
15:00 Nyimbo Na. 29 ndi Pemphero