Gwiritsani Ntchito Timapepala Ngati:
• Mwininyumba wakana kukambirana naye
• Mwininyumba watanganidwa
• M’malo ena simunapeze mwininyumba
• Mukulalikira mwamwayi
• Mukufuna kuyamba kukambirana ndi anthu
• Mukuphunzitsa ana kulalikira
• Mukusonyeza ophunzira Baibulo anu mmene angalalikirire kwa anzawo
• Mukufuna kuyambitsa phunziro la Baibulo