Ndandanda ya Mlungu wa May 4
MLUNGU WOYAMBIRA MAY 4
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cl-CN mutu 18 ndime 16-24 ndi bokosi
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Eksodo 23-26
Na. 1: Eksodo 24:1-18
Na. 2: Kodi Chofunika Kwambiri Ndi Chiyani? (lr-CN mutu 16)
Na. 3: Kodi Akhristu Oona Tingawadziwe Bwanji Masiku Ano? (rs-CN tsa. 167 ndime 1–tsa. 168 ndime 2)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph.5: Zilengezo.
Mph.5: “Gwiritsani Ntchito Timapepala.” Limbikitsani abale kuti azigawira timapepala mpata ukapezeka.
Mph.13: “Kodi Mumayamikira Mabuku Athu?” Nkhani yokambirana mwa mafunso ndi mayankho.
Mph.12: Kufunika Kosonyeza Ena Chidwi. Nkhani yokambirana ndi omvera kuchokera pa Mateyo 8:2, 3 ndi Luka 7:11-15. N’chifukwa chiyani anthu amamvetsera kwambiri tikawasonyeza chidwi? Kodi tingadziwe bwanji nkhani imene mwininyumba ali nayo chidwi kapena zinthu zimene zikumudetsa nkhawa? Kodi tingasonyeze bwanji chidwi tikakumana ndi munthu wachikulire, wachinyamata, wophunzira ku koleji, kholo, kapena munthu amene akudwala, mwinanso amene wachibale wake wamwalira?