Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 September tsamba 6
  • “Yehova ndi Wamkulu ndi Woyenera Kutamandidwa Kwambiri”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Yehova ndi Wamkulu ndi Woyenera Kutamandidwa Kwambiri”
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
  • Nkhani Yofanana
  • Ukulu wa Yehova ndi Wosasanthulika
    Nsanja ya Olonda—2004
  • Yehova Amafunikira Chitamando Chosatha
    Nsanja ya Olonda​—1990
  • Chikondi Chokhulupirika cha Yehova N’chachikulu
    Nsanja ya Olonda—2004
  • Dalitsani Dzina Loyera la Yehova!
    Nsanja ya Olonda​—1990
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 September tsamba 6

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MASALIMO 142-150

“Yehova ndi Wamkulu ndi Woyenera Kutamandidwa Kwambiri”

145:1-5

Kumwamba kumene kuli nyenyezi

Davide anaona kuti ukulu wa Yehova ndi wosasanthulika ndipo zimenezi zinachititsa kuti azitamanda Yehova

145:10-12

Mofanana ndi Davide, atumiki a Yehova okhulupirika amayesetsa kuuza ena ntchito zodabwitsa za Yehova

Banja likuyang’ana kumwamba komwe kuli nyenyezi

145:14

Munthu akuthandiza mnzake pomugwira dzanja

Davide ankakhulupirira kuti Yehova amafunitsitsa kuthandiza atumiki ake

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena