Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 November tsamba 1
  • Zitsanzo za Ulaliki

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zitsanzo za Ulaliki
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • NSANJA YA OLONDA
  • KUPHUNZITSA CHOONADI
  • N’CHIFUKWA CHIYANI TIYENERA KUPHUNZIRA BAIBULO? (Vidiyo)
  • LEMBANI ULALIKI WANUWANU
  • Zitsanzo za Ulaliki
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Zitsanzo za Ulaliki
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
  • Zitsanzo za Ulaliki
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Zitsanzo za Ulaliki
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 November tsamba 1
Alongo akulalikira mzimayi wina m’chinenero cha Chitsotsilu ku Chiapas m’dziko la Mexico

Apainiya akulalikira m’chinenero cha Chitsotsilu ku Chiapas m’dziko la Mexico

Zitsanzo za Ulaliki

NSANJA YA OLONDA

Nsanja ya Olonda Na. 6 2016 | Masomphenya Otithandiza Kumvetsa za Kumwamba

Funso: Kodi mungayankhe bwanji munthu wina atakufunsani kuti kumwamba n’kotani?

Lemba: Yoh. 8:23

Perekani Magaziniyo: Nsanja ya Olonda iyi ikufotokoza zimene Yesu ndiponso Atate ake ananena zokhudza kumwamba.

KUPHUNZITSA CHOONADI

Baibulo lotsegula

Funso: Kodi mukuona kuti zimene Baibulo linaneneratu palemba ili zikuchitikadi masiku ano?

Lemba: 2 Tim. 3:1-5

Zoona Zake: Popeza kuti ulosi wa m’Baibulo wokhudza masiku otsiriza ukukwaniritsidwa, sitingakayikire kuti ulosi wokhudza zinthu zabwino zimene tikuyembekezera m’tsogolo udzakwaniritsidwanso.

N’CHIFUKWA CHIYANI TIYENERA KUPHUNZIRA BAIBULO? (Vidiyo)

N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo? (vidiyo)

Mawu Oyamba: Tikuonetsa anthu vidiyo yomwe imawathandiza kudziwa komwe angapeze mayankho a mafunso ofunika kwambiri. [Onetsani vidiyo.]

Perekani Buku: Bukuli limafotokoza zimene Baibulo limanena zokhudza zimene Mulungu adzachite pothetsa mavuto a m’dzikoli. [Perekani buku lakuti, Zimene Baibulo Limaphunzitsa.]

LEMBANI ULALIKI WANUWANU

Potengera zitsanzozi, konzani njira imene mungagwiritse ntchito.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena