Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 January tsamba 5
  • Hezekiya Anadalitsidwa Chifukwa cha Chikhulupiriro Chake

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Hezekiya Anadalitsidwa Chifukwa cha Chikhulupiriro Chake
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Nkhani Yofanana
  • Mngelo wa Yehova Anateteza Hezekiya
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • “Usaope Ndidzakuthandiza”
    Nsanja ya Olonda—2010
  • Mulungu Athandiza Mfumu Hezekiya
    Bukhu Langa la Nkhani za Baibulo
  • Kodi Abusa 7 ndi Atsogoleri 8 Akuimira Ndani Masiku Ano?
    Nsanja ya Olonda—2013
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 January tsamba 5

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YESAYA 34-37

Hezekiya Anadalitsidwa Chifukwa cha Chikhulupiriro Chake

Rabisake ndi asilikali ake ali kunja kwa mpanda wa Yerusalemu

Senakeribu, yemwe anali mfumu ya Asuri, anatumiza Rabisake ku Yerusalemu kuti akakakamize Ayuda amumzindawo kuti angodzipereka okha. Asuriwo ananena mfundo zambiri zoopseza n’cholinga choti Ayuda achite mantha n’kudzipereka okha kwa Asuri popanda kumenya nkhondo

  • Asilikali a Asuri aima kunja kwa mpanda wa Yerusalemu

    Anawauza kuti adzasowa owathandiza. Aiguputo sangakuthandizeni.—Yes. 36:6

  • Anthu akukayikira

    Anawapangitsa kukayikira za Yehova. Yehova sakumenyerani nkhondo chifukwa sakusangalala nanu.—Yes. 36:7, 10

  • Asilikali a Asuri

    Anawaopseza. Musaganize n’komwe zoti mungalimbane ndi asilikali amphamvu a Asuri.—Yes. 36:8, 9

  • Nyumba yaikulu komanso munda

    Anawanyengerera. Mukadzipereka nokha kwa Asuri zinthu zikuyenderani bwino pa moyo wanu.—Yes. 36:16, 17

Hezekiya sanasiye kukhulupirira Yehova

37:1, 2, 14-20, 36

  • Anayesetsa kuchita zinthu mwanzeru pokonzekera kubwera kwa Asuri

  • Anapemphera kwa Yehova kuti awapulumutse komanso analimbikitsa anthu onse kuti azipemphera

  • Yehova anadalitsa Hezekiya chifukwa cha chikhulupiriro chake moti anatumiza mngelo kuti akaphe asilikali a Asuri okwana 185,000 usiku umodzi wokha

    Hezekiya akupemphera ndipo mngelo wanyamula lupanga
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena