Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 August tsamba 1
  • Zitsanzo za Ulaliki

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zitsanzo za Ulaliki
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • GALAMUKANI!
  • KUPHUNZITSA CHOONADI
  • UTHENGA WABWINO WOCHOKERA KWA MULUNGU
  • LEMBANI ULALIKI WANUWANU
  • Zitsanzo za Ulaliki
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
  • Zitsanzo za Ulaliki
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Zitsanzo za Ulaliki
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Zitsanzo za Ulaliki
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 August tsamba 1
Ofalitsa awiri akugawira kabuku ka Uthenga Wabwino kwa mayi wina ku Azerbaijan

Ofalitsa akugawira kabuku ka Uthenga Wabwino ku Azerbaijan

Zitsanzo za Ulaliki

GALAMUKANI!

Galamukani! Na. 4 2017 | Kodi Inuyo Mumatanganidwa Kwambiri?

Funso: Kodi tingatani kuti tizigwiritsa ntchito bwino nthawi?

Lemba: Mlal. 4:6

Perekani Magaziniyo: Galamukani! iyi ili ndi mfundo zothandiza zokhudza mmene tingagwiritsire ntchito bwino nthawi.

KUPHUNZITSA CHOONADI

Baibulo lotsegula

Funso: Kodi Mulungu anatilenga chifukwa chiyani?

Lemba: Sal. 37:29

Zoona Zake: Mulungu analenga anthu n’cholinga choti azikhala ndi moyo padzikoli mpaka kalekale.

UTHENGA WABWINO WOCHOKERA KWA MULUNGU

Uthenga Wabwino Wochokera kwa Mulungu!

Funso: Kodi mukuganiza kuti uthenga wabwino tingaupeze kuti? [Onetsani vidiyo yakuti Kodi Mungakonde Kumva Uthenga Wabwino?]

Lemba: Yes. 52:7

Perekani Kabuku: Kabuku aka kali ndi “uthenga wabwino wa zinthu zabwino” chifukwa muli mfundo za m’Baibulo.

LEMBANI ULALIKI WANUWANU

Potengera zitsanzozi, konzani njira imene mungagwiritse ntchito.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena