Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 August tsamba 5
  • Udindo Waukulu wa Mlonda

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Udindo Waukulu wa Mlonda
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Nkhani Yofanana
  • “Ine Ndakuika Kuti Ukhale Mlonda”
    Yehova Wabwezeretsa Kulambira Koyera
  • Mvetserani—Mlonda wa Yehova Akulankhula!
    Nsanja ya Olonda—1988
  • Mafunso Ochokera kwa Oŵerenga
    Nsanja ya Olonda—2003
  • Mmene Yehova Amatithandizira Kukwaniritsa Utumiki Wathu
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2022
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 August tsamba 5

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EZEKIELI 32-34

Udindo Waukulu wa Mlonda

Anthu amene ankagwira ntchito ya ulonda ankakhala pamwamba pa mpanda kapena pansanja ndipo ankachenjeza anthu ngati kukubwera zoopsa. Yehova mophiphiritsira anasankha Ezekieli kuti akhale “mlonda wa nyumba ya Isiraeli.”

Mlonda waima pampanda wa mzinda
  • Mlonda akupereka chenjezo

    33:7

    Ezekieli anachenjeza Aisiraeli kuti adzawonongedwa ngati sasiya kuchita zoipa

    Kodi masiku ano timalengeza uthenga wotani wochokera kwa Yehova?

  • Asilikali alowa mumzinda mlonda atalephera kupereka chenjezo

    33:9, 14-16

    Ngati akanapereka chenjezo, Ezekieli akanapulumutsa moyo wake komanso wa anthu ena

    Kodi n’chiyani chingatilimbikitse kuti tizilengeza mwachangu uthenga umene Yehova watipatsa?

Mlungu uno ndiyesetsa kuti ndilalikire kwa . . .

  • mnzanga wa kusukulu

  • mnzanga wa kuntchito

  • wachibale wanga amene si wa Mboni

  • anthu ena:

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena