CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MALIKO 1-2
“Machimo Ako Akhululukidwa”
Kodi tikuphunzirapo chiyani pa chozizwitsa chimenechi?
Timadwala chifukwa chakuti tinatengera uchimo
Yesu ali ndi mphamvu zokhululukira machimo komanso kuchiritsa odwala
Mu Ufumu wa Mulungu, Yesu adzathetsa uchimo komanso matenda
Kodi lemba la Maliko 2:5-12 lingandithandize bwanji kupirira ndikamadwala?