Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 January tsamba 6
  • Paulo Anapita ku Roma

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Paulo Anapita ku Roma
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Nkhani Yofanana
  • Paulo Anatumizidwa ku Roma
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • Mafunso Ochokera kwa Oŵerenga
    Nsanja ya Olonda—2004
  • “Palibe Amene Ataye Moyo Wake”
    ‘Kuchitira Umboni Mokwanira za Ufumu wa Mulungu’
  • Paulo Alaka Mavuto
    Nsanja ya Olonda—1999
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 January tsamba 6

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MACHITIDWE 27-28

Paulo Anapita ku Roma

27:23, 24; 28:1, 2, 16, 17

Ngakhale kuti Paulo anali atamangidwa, sanasiye kuuza ena zimene ankakhulupirira. Pamene anali mungalawa analalikira kwa oyendetsa komanso anthu ena amene anakwera ngalawayo. N’zosakayikitsa kuti ngalawayo itasweka pachilumba cha Melita, iye anapeza mwayi wouza uthenga wabwino anthu amene anawachiritsa. Patangodutsa masiku atatu atafika ku Roma, anasonkhanitsa akuluakulu a Ayuda kuti awalalikire. Komanso pa zaka ziwiri zomwe anali pa ukaidi wosachoka panyumba, ankalalikira kwa anthu amene ankabwera kudzamuona.

Kodi mungatani kuti muzilalikira uthenga wabwino ngakhale kuti mukukumana ndi mavuto osiyanasiyana?

Paulo akulalikira akuluakulu a Ayuda ku Roma atamangiriridwa kwa msilikali; mmene Paulo anayendera kuchokera ku Kaisareya kupita ku Roma
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena