CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AROMA 1-3
Pitirizani Kuphunzitsa Chikumbumtima Chanu
Chikumbumtima chathu chingatithandize kusankha bwino zochita ngati . . .
timachiphunzitsa pogwiritsa ntchito mfundo za m’Baibulo
timachimvera chikamatikumbutsa mfundozo
timapempha mzimu woyera kuti utithandize kulimbana ndi matupi athu ochimwawa.—Aroma 9:1