Mkulu akuphunzitsa m’bale wachinyamata ntchito zapampingo
Zimene Tinganene
●○○ ULENDO WOYAMBA
Funso: Kodi Mulungu ndi amene amachititsa kuti tizivutika?
Lemba: Yobu 34:10
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi n’chiyani chimachititsa kuti tizivutika?
○●○ ULENDO WOBWEREZA WOYAMBA
Funso: Kodi n’chiyani chimachititsa kuti tizivutika?
Lemba: 1 Yoh. 5:19
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi Mulungu adzathetsa bwanji mavuto onse amene Satana anayambitsa?
○○● ULENDO WOBWEREZA WACHIWIRI
Funso: Kodi Mulungu adzathetsa bwanji mavuto onse amene Satana anayambitsa?
Lemba: Mat. 6:9, 10
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi Ufumu wa Mulungu n’chiyani?