CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | 1 YOHANE 1-5
Musamakonde Dziko Kapena Zinthu za M’dziko
Satana amagwiritsa ntchito zinthu zitatu zotsatirazi zomwe dziko limalimbikitsa pofuna kutichititsa kuti tisiye kutumikira Yehova. Kodi zinthu zimenezi mungazifotokoze bwanji?
“Chilakolako cha thupi”
“Chilakolako cha maso”
“Kudzionetsera ndi zimene munthu ali nazo”