Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 March tsamba 10
  • “Ine Ndine . . . Cholowa Chako”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Ine Ndine . . . Cholowa Chako”
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nkhani Yofanana
  • Yehova Amatsogolera Anthu Ake
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Samalani Kuti Musakhale Wonyada Ndi Wodzidalira
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Muzifunsira Nzeru kwa Yehova
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Yehova Ndi Cholowa Changa
    Nsanja ya Olonda—2011
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 March tsamba 10

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Ine Ndine . . . Cholowa Chako”

Yehova anapatsa ansembe ndi Alevi mwayi wapadera wochita utumiki wofunika kwambiri (Nu 18:6, 7)

Anthu a fuko la Levi sanalandire cholowa cha malo. Cholowa chawo anali Yehova (Nu 18:20, 24; w11 9/15 13 ¶9)

Aisiraeli ankapereka chakhumi pa zokolola zawo kuti chizithandiza Alevi ndi ansembe (Nu 18:21, 26, 27; w11 9/15 7 ¶4)

Yehova analonjeza Alevi ndi ansembe kuti aziwapatsa zofunika pa moyo. Sitiyenera kukayikira kuti Yehova adzatisamalira ngati titadzimana zinthu zina n’cholinga choti tizimutumikira.

Yehova amasamalira atumiki ake. 1. Mlongo akuika ndalama mu envulopu. 2. Envulopu ili pansi pa chitseko. 3. Mayi amene akulera yekha mwana wakumbatira mwana wakeyo ndipo akuyang’ana ndalama zomwe zili mu envulopu.
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena