Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 July tsamba 13
  • Mmene Chilengedwe Chimasonyezera Kuti Mulungu Ndi Wachikondi

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mmene Chilengedwe Chimasonyezera Kuti Mulungu Ndi Wachikondi
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nkhani Yofanana
  • Muziphunzira Zambiri Zokhudza Yehova Poona Chilengedwe Chake
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2023
  • Muzigwiritsa Ntchito Chilengedwe Pophunzitsa Ana Anu Zokhudza Yehova
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2023
  • Kodi Zinthu Zinachita Kulengedwa?—Gawo 3: N’chifukwa Chiyani Ndiyenera Kukhulupirira Kuti Zinthu Zinachita Kulengedwa?
    Zimene Achinyamata Amafunsa
  • Kodi Mumaona Makhalidwe a Mulungu Osaoneka ndi Maso?
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 July tsamba 13
Bambo akulozera mwana wake mbalame yomwe yatera mumtengo pamene akulalikira nyumba ndi nyumba.

Popeza kuti Yehova anasonyeza kuti amatikonda kwambiri kudzera m’chilengedwechi, sitiyenera kukaikira kuti iye adzatidalitsa kwambiri tikamayesetsa kumutumikira mwakhama

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Mmene Chilengedwe Chimasonyezera Kuti Mulungu Ndi Wachikondi

Nthawi zambiri timakhala otanganidwa ndi zochita zathu za tsiku ndi tsiku moti timalephera kupeza nthawi yoganizira mmene chilengedwe chimasonyezera kuti Yehova ndi wachikondi komanso wowolowa manja. Koma Yesu anatilimbikitsa kuti tizichita chidwi ndi chilengedwe komanso kuganizira zimene chikutiphunzitsa zokhudza Yehova.​—Mt 6:25, 26.

ONERANI VIDIYO YAKUTI CHILENGEDWE CHIMASONYEZA KUTI YEHOVA NDI WACHIKONDI, NDIPO KENAKO YANKHANI MAFUNSO OTSATIRAWA:

Kodi zinthu zotsatirazi zakuphunzitsani chiyani zokhudza chikondi cha Yehova kwa anthufe?:

  • tinthu tomwe timapanga zinthu za padzikoli

  • mlengalenga

  • udzu

  • mmene nyama zinalengedwera

  • kununkhiza, kulawa, kumva, kuona, kukhudza

  • ubongo

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena