Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 January tsamba 14
  • Kodi Mfumu Yanu ndi Ndani?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mfumu Yanu ndi Ndani?
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • Kumvera Kumaposa Nsembe
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Mmene Davide Ankamenyera Nkhondo
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Kudzikuza Kumabweretsa Manyazi
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Dzilimbitseni mwa Yehova Mulungu Wanu
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 January tsamba 14
Mneneri Samueli akuloza kumwamba pamene akulankhula ndi Aisiraeli ena.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kodi Mfumu Yanu ndi Ndani?

Aisiraeli anapempha mfumu mwamwano (1Sa 8:4, 5; it-2 163 ¶1)

Aisiraeli sankakhutira kuti Yehova ndiye Wolamulira wawo wosaoneka (1Sa 8:7, 8; w11 1/1 27 ¶1)

Yehova anawachenjeza za mavuto amene adzakumane nawo chifukwa cha zomwe ankafuna (1Sa 8:9, 18; w10 1/15 30 ¶9)

Nthawi zonse Yehova amasonyeza mphamvu zake pa zinthu zimene analenga. Iye amalamulira bwino anthu ake komanso amawalemekeza. Tikamamumvera komanso kukhala kumbali ya ulamuliro wake, tidzapeza madalitso osatha.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ineyo pandekha, ndingasonyeze bwanji kuti ndimagonjera ulamuliro wa Yehova?’

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena