CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Barizilai Anali Wodzichepetsa
Barizilai anapatsidwa mwayi wa utumiki ndi Mfumu Davide (2Sa 19:32, 33; w07 7/15 14 ¶5)
Chifukwa choti Barizilai anali wodzichepetsa, anakana mwayiwu mwaulemu (2Sa 19:34, 35; w07 7/15 14 ¶7)
Khalani odzichepetsa ngati Barizilai (w07 7/15 15 ¶1-2)
Kudzichepetsa kumatithandiza kudziwa zinthu zimene sitingakwanitse kuchita. Tiyenera kukhala odzichepetsa kuti tizisangalatsa Yehova. (Mik 6:8) Kodi kukhala ndi khalidwe limeneli kumatithandiza bwanji?