Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 July tsamba 8
  • Kodi Mumaphunzirapo Kanthu Mukalakwitsa Zinazake?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mumaphunzirapo Kanthu Mukalakwitsa Zinazake?
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Ndizitani Ndikalakwitsa Zinazake?
    Mayankho a Mafunso 10 Omwe Achinyamata Amadzifunsa
  • Kodi Ndizitani Ndikalakwitsa Zinazake?
    Zimene Achinyamata Amafunsa
  • Muzitsanzira Mmene Yehova Amagwiritsira Ntchito Udindo Wake
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Kodi Nkuvomereranji Cholakwa?
    Nsanja ya Olonda—1993
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 July tsamba 8
Mlongo akuwerenga Baibulo ndipo akuganizira zimene Adoniya anachita. Zithunzi: 1. Adoniya wagwira nyanga ya guwa la nsembe. 2. Adoniya akunyengerera Batiseba.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kodi Mumaphunzirapo Kanthu Mukalakwitsa Zinazake?

[Onerani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la 1 Mafumu.]

Adoniya anasonyezedwa chifundo atachita zinthu modzikweza pofuna kuti akhale mfumu (1Mf 1:5, 52, 53; it-2 987 ¶4)

Adoniya sanaphunzirepo kanthu pa zimene analakwitsa ndipo anakumana ndi mavuto (1Mf 2:15-17, 22, 23; it-1 49)

Munthu wanzeru amaphunzirapo kanthu akalakwitsa zinazake. Komanso kuwonjezera pamenepo amaphunziranso kanthu pa zimene ena alakwitsa.​—1Ak 10:11.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena