Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 March tsamba 2
  • Kulambira kwa Pakachisi Kunali kwa Dongosolo

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kulambira kwa Pakachisi Kunali kwa Dongosolo
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Utumiki wa Alevi
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Mfundo Zothandiza Kuweruza Milandu Mwachilungamo
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Kodi Chilamulo Chinkasonyeza Bwanji Kuti Yehova Amaganizira Anthu Osauka?
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Zimene Tingaphunzire pa Zomwe Zinkachitika pa Msasa wa Aisiraeli
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 March tsamba 2

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kulambira kwa Pakachisi Kunali kwa Dongosolo

Mfumu Davide inakonza zoti Alevi ndi ansembe azitumikira pakachisi (1Mb 23:6, 27, 28; 24:1, 3; it-2 241, 686)

Akatswiri oimba komanso ophunzira kuimba anapatsidwa utumiki wokonza nyimbo (1Mb 25:1, 8; it-2 451-452)

Alevi anapatsidwa utumiki woyang’anira chuma, ena anali alonda a pachipata komanso ena anapatsidwa maudindo osiyanasiyana (1Mb 26:16-20; it-1 898)

Abale ndi alongo ali mu Nyumba ya Ufumu misonkhano ya mpingo isanayambe. 1. Akupatsana moni komanso akucheza. 2. M’bale akusonyeza mlongo chinthu china chimene chaikidwa pa bolodi la zilengezo. 3. Mlongo akuponya ndalama m’bokosi la zopereka. 4. M’bale ali kuseri kwa shelefu ndipo akupereka mabuku kwa mlongo. 5. M’bale akukweza maikolofoni ku pulatifomu. 6. M’bale ndi mwana wake akusesa.

Timalambira Yehova mwadongosolo chifukwa iye ndi Mulungu wadongosolo.​—1Ak 14:33.

FUNSO LOFUNIKA KULIGANIZIRA: Kodi mpingo wa Chikhristu masiku ano umasonyeza bwanji kuti umalambira Yehova mwadongosolo?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena