Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 May tsamba 11
  • Muzilimbikitsa Abale ndi Alongo Anu Akakumana ndi Mavuto

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Muzilimbikitsa Abale ndi Alongo Anu Akakumana ndi Mavuto
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Zimene Mungachite Kuti Zinthu Zizikuyenderani Bwino
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Muzitsanzira Yehova Yemwe Ndi Wosakondera
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Yehova Amadalitsa Anthu Achikhulupiriro
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • “Khulupirirani Yehova Mulungu Wanu”
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 May tsamba 11

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Muzilimbikitsa Abale ndi Alongo Anu Akakumana ndi Mavuto

Senakeribu anazungulira mzinda wa Yuda ndipo anaopseza Yerusalemu (2Mb 32:1; it-1 204 ¶5)

Hezekiya anachita zinthu zothandiza kuti ateteze mzinda wa Yerusalemu (2Mb 32:2-5; w13 11/15 19 ¶12)

Hezekiya analimbikitsa anthu a Mulungu ndi mawu ake (2Mb 32:6-8; w13 11/15 19 ¶13)

Abale akupereka thandizo kwa mayi ndi mwana wake.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndingathandize bwanji abale ndi alongo anga panthawi ya mavuto?’

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena