Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 May tsamba 14
  • Muzilola Kuti Yehova Azikugwiritsani Ntchito

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Muzilola Kuti Yehova Azikugwiritsani Ntchito
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • “Musakalowerere Ntchito Yomanga”
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Kodi Mukukumbukira?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2022
  • Kusamvera Kumapweteketsa
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Zochita za Ezara Zinachititsa Kuti Dzina la Yehova Lilemekezedwe
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 May tsamba 14

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Muzilola Kuti Yehova Azikugwiritsani Ntchito

[Onerani vidiyo ya Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Ezara.]

Yehova analimbikitsa mtima wa Mfumu Koresi kuti akamasule Aisiraeli (Eza 1:1-3; w22.03 14 ¶1)

Yehova analimbikitsa mtima wa anthu ake kuti akamangenso kachisi (Eza 1:5; w17.10 26 ¶2)

M’bale akugwiritsa ntchito Baibulo polimbikitsa m’bale wina komanso mkazi wake amene wavulala kwambiri ndipo ali m’chipatala.

Ngati mungadzipereke, Yehova akhoza kuchititsa kuti mukhale chilichonse chimene iye akufuna kuti akwaniritse cholinga chake.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena