Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 July tsamba 2
  • “Musakalowerere Ntchito Yomanga”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Musakalowerere Ntchito Yomanga”
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Mukukumbukira?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2022
  • Muzilola Kuti Yehova Azikugwiritsani Ntchito
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Musamasiye Akhristu Anzanu
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Kodi Ndi pa Nthawi Iti Pamene Tiyenera Kudalira Yehova?
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 July tsamba 2

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Musakalowerere Ntchito Yomanga”

Mkulu wa Ansembe Yesuwa (Yoswa) komanso Bwanamkubwa Zerubabele, anatsogolera pa ntchito yomanganso kachisi ngakhale kuti ntchitoyo inaletsedwa (Eza 5:1, 2; w22.03 18 ¶13)

Pamene otsutsa anafunsa kuti ndi ndani amene anawaloleza kugwira ntchitoyo, Ayuda anatchula za lamulo limene Koresi anapereka (Eza 5:3, 17; w86 2/1 29, bokosi ¶2-3)

Mfumu inatsimikizira kuti inaperekadi lamulolo ndipo inalamula otsutsawo kuti asalowerere pa ntchitoyo (Eza 6:7, 8; w22.03 15 ¶7)

Mlongo akuonera pulogalamu ya JW Broadcasting ndipo m’maganizo mwake akuona Zerubabele komanso Mkulu wa Ansembe Yesuwa akutsogolera Aisiraeli anzawo pa ntchito yomanganso kachisi.

FUNSO LOFUNIKA KULIGANIZIRA: Kodi nkhani ya m’Baibuloyi ikutithandiza bwanji kutsatira malangizo ochokera kwa anthu omwe Yehova anawasankha kuti azititsogolera ngakhale kuti sitikumvetsa malangizowo?​—w22.03 18 ¶16.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena