-
Genesis 40:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Mubasiketi yapamwamba munali mikate yosiyanasiyana ya Farao, ndipo mbalame zimadya mikate imene inali mʼbasiketimo pamutu panga.”
-