Genesis 40:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Munsengwa yapamwambayo munali mikate yosiyanasiyana ya Farao,+ ndipo mbalame+ zinali kudya mikateyo munsengwayo pamutu panga.”
17 Munsengwa yapamwambayo munali mikate yosiyanasiyana ya Farao,+ ndipo mbalame+ zinali kudya mikateyo munsengwayo pamutu panga.”