-
Genesis 45:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Koma atamufotokozera zonse zimene Yosefe ananena, ndiponso ataona ngolo zimene Yosefe anatumiza kuti zidzamutenge, Yakobo bambo awo anayamba kusangalala.
-