Genesis 45:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma atamufotokozera mawu onse amene Yosefe ananena, ndiponso ataona ngolo zimene Yosefe anatumiza kuti zidzam’tenge, mtima wa Yakobo bambo awo unayamba kubwereramo.+
27 Koma atamufotokozera mawu onse amene Yosefe ananena, ndiponso ataona ngolo zimene Yosefe anatumiza kuti zidzam’tenge, mtima wa Yakobo bambo awo unayamba kubwereramo.+