Genesis 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Komanso pa zamoyo zilizonse zouluka mumlengalenga, utengepo zokwanira 7,* chachimuna ndi chachikazi, kuti zisungike padziko lonse lapansi.+
3 Komanso pa zamoyo zilizonse zouluka mumlengalenga, utengepo zokwanira 7,* chachimuna ndi chachikazi, kuti zisungike padziko lonse lapansi.+