Ekisodo 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako Yehova anauza Mose ndi Aroni kuti: “Tengani phulusa* la mu uvuni lodzaza manja anu awiri ndipo Mose aliponye mʼmwamba Farao akuona.
8 Kenako Yehova anauza Mose ndi Aroni kuti: “Tengani phulusa* la mu uvuni lodzaza manja anu awiri ndipo Mose aliponye mʼmwamba Farao akuona.