Ekisodo 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako Yehova anauza Mose ndi Aroni kuti: “Tengani mwaye wa mu uvuni wodzaza manja anu awiri,+ ndipo Mose auponye m’mwamba, Farao akuona.
8 Kenako Yehova anauza Mose ndi Aroni kuti: “Tengani mwaye wa mu uvuni wodzaza manja anu awiri,+ ndipo Mose auponye m’mwamba, Farao akuona.