Ekisodo 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Aisiraeli ataona tinthu timeneti anayamba kufunsana kuti: “Nʼchiyani ichi?” chifukwa sankadziwa kuti chinali chiyani. Mose anawauza kuti: “Ndi chakudya chimene Yehova wakupatsani.+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:15 Nsanja ya Olonda,8/15/1999, tsa. 25
15 Aisiraeli ataona tinthu timeneti anayamba kufunsana kuti: “Nʼchiyani ichi?” chifukwa sankadziwa kuti chinali chiyani. Mose anawauza kuti: “Ndi chakudya chimene Yehova wakupatsani.+