Ekisodo 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ana a Isiraeli ataona tinthu timeneti anayamba kufunsana kuti: “N’chiyani ichi?” Chifukwa sanadziwe kuti chinali chiyani. Pamenepo Mose anawauza kuti: “Ndi chakudya chimene Yehova wakupatsani.+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:15 Nsanja ya Olonda,8/15/1999, tsa. 25
15 Ana a Isiraeli ataona tinthu timeneti anayamba kufunsana kuti: “N’chiyani ichi?” Chifukwa sanadziwe kuti chinali chiyani. Pamenepo Mose anawauza kuti: “Ndi chakudya chimene Yehova wakupatsani.+