Ekisodo 21:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ngati ngʼombe yagunda mwamuna kapena mkazi, munthuyo nʼkumwalira, ngʼombeyo iziponyedwa miyala nʼkuphedwa+ ndipo nyama yake sikuyenera kudyedwa. Zikatero mwiniwake wa ngʼombeyo sakuyenera kulangidwa. Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:28 Nsanja ya Olonda,4/15/2010, tsa. 29
28 Ngati ngʼombe yagunda mwamuna kapena mkazi, munthuyo nʼkumwalira, ngʼombeyo iziponyedwa miyala nʼkuphedwa+ ndipo nyama yake sikuyenera kudyedwa. Zikatero mwiniwake wa ngʼombeyo sakuyenera kulangidwa.