Ekisodo 21:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Ng’ombe ikagunda mwamuna kapena mkazi, munthuyo n’kumwalira, ng’ombeyo iziponyedwa miyala ndi kuphedwa+ ndithu, ndipo nyama yake isadyedwe. Zikatero mwiniwake wa ng’ombeyo sayenera kulangidwa. Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:28 Nsanja ya Olonda,4/15/2010, tsa. 29
28 “Ng’ombe ikagunda mwamuna kapena mkazi, munthuyo n’kumwalira, ng’ombeyo iziponyedwa miyala ndi kuphedwa+ ndithu, ndipo nyama yake isadyedwe. Zikatero mwiniwake wa ng’ombeyo sayenera kulangidwa.