-
Ekisodo 21:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Koma ngati ngʼombeyo inkadziwika kuti ili ndi chizolowezi chogunda zinzake, koma mwiniwake sankaiyangʼanira, azipereka ngʼombe kulipira ngʼombe, ndipo azitenga yakufayo.”
-