Ekisodo 21:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Kapena ngati ng’ombe inali kudziwika ndi chizolowezi chogunda zinzake, koma mwiniwake sanali kuiyang’anira,+ azipereka ndithu+ ng’ombe kulipira ng’ombe, ndipo azitenga yakufayo.
36 Kapena ngati ng’ombe inali kudziwika ndi chizolowezi chogunda zinzake, koma mwiniwake sanali kuiyang’anira,+ azipereka ndithu+ ng’ombe kulipira ng’ombe, ndipo azitenga yakufayo.