Ekisodo 30:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “Upange guwa lansembe zofukiza.+ Ulipange ndi matabwa amthethe.+