Ekisodo 33:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiye ngati mwandikomeradi mtima, chonde ndidziwitseni njira zanu+ kuti ndikudziweni komanso kuti mupitirize kundikomera mtima. Kumbukiraninso kuti mtundu uwu ndi anthu anu.”+
13 Ndiye ngati mwandikomeradi mtima, chonde ndidziwitseni njira zanu+ kuti ndikudziweni komanso kuti mupitirize kundikomera mtima. Kumbukiraninso kuti mtundu uwu ndi anthu anu.”+