Ekisodo 33:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano ngati mwandikomera mtima,+ chonde ndidziwitseni njira zanu,+ kuti ndikudziweni, kutinso mundikomere mtima. Ndipo kumbukirani kuti mtundu uwu ndi anthu anu.”+
13 Tsopano ngati mwandikomera mtima,+ chonde ndidziwitseni njira zanu,+ kuti ndikudziweni, kutinso mundikomere mtima. Ndipo kumbukirani kuti mtundu uwu ndi anthu anu.”+