Ekisodo 34:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndipo ukonzeke kuti mawa mʼmawa ukakwere phiri la Sinai nʼkukakhala pamaso panga kumeneko pamwamba pa phirilo.+
2 Ndipo ukonzeke kuti mawa mʼmawa ukakwere phiri la Sinai nʼkukakhala pamaso panga kumeneko pamwamba pa phirilo.+